Ezekieli 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mkangowo unkasaka nyama pakati pa nsanja zawo zokhala ndi mipanda yolimba ndipo unawononga mizinda yawo.Moti mʼdziko labwinjalo munkangomveka kubangula kwa mkangowo.+
7 Mkangowo unkasaka nyama pakati pa nsanja zawo zokhala ndi mipanda yolimba ndipo unawononga mizinda yawo.Moti mʼdziko labwinjalo munkangomveka kubangula kwa mkangowo.+