-
Ezekieli 19:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mitundu ya anthu imene inkakhala mʼzigawo zozungulira inabwera kudzauukira ndipo inautchera ukonde,
Mkangowo unagwera mʼdzenje lawo.
-