-
Ezekieli 19:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako anaukola ndi ngowe nʼkuuika mʼkakhola ndipo anapita nawo kwa mfumu ya Babulo.
Atafika nawo anautsekera kuti mawu ake asadzamvekenso mʼmapiri a ku Isiraeli.
-