Ezekieli 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma mtengowo unazulidwa mwaukali+ nʼkuponyedwa pansi,Ndipo mphepo yakumʼmawa inaumitsa zipatso zake. Nthambi zake zimene zinali zolimba zinathyoledwa nʼkuuma+ ndipo zinawotchedwa ndi moto.+
12 Koma mtengowo unazulidwa mwaukali+ nʼkuponyedwa pansi,Ndipo mphepo yakumʼmawa inaumitsa zipatso zake. Nthambi zake zimene zinali zolimba zinathyoledwa nʼkuuma+ ndipo zinawotchedwa ndi moto.+