Ezekieli 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Motowo unafalikira kuchokera kunthambi* zake ndipo unawotcha mphukira ndi zipatso zake,Ndipo mtengowo unalibenso nthambi zolimba komanso ndodo ya olamulira.+ Imeneyi ndi nyimbo yoimba polira ndipo idzakhala nyimbo yotchuka.’”
14 Motowo unafalikira kuchokera kunthambi* zake ndipo unawotcha mphukira ndi zipatso zake,Ndipo mtengowo unalibenso nthambi zolimba komanso ndodo ya olamulira.+ Imeneyi ndi nyimbo yoimba polira ndipo idzakhala nyimbo yotchuka.’”