-
Ezekieli 20:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mʼchaka cha 7, mʼmwezi wa 5, pa tsiku la 10 la mweziwo, akuluakulu ena a Isiraeli anabwera nʼkudzakhala pansi pafupi ndi ine kuti adzafunsire kwa Yehova.
-