-
Ezekieli 20:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma a nyumba ya Isiraeli anandipandukira mʼchipululu.+ Iwo sanatsatire malamulo anga ndipo anakana zigamulo zanga zimene munthu akamazitsatira, zimamuthandiza kuti akhale ndi moyo. Sabata langa analidetsa kwambiri. Choncho ndinatsimikiza mtima kuti ndiwatsanulire mkwiyo wanga mʼchipululu kuti onse ndiwawonongeretu.+
-