Ezekieli 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndinauza ana awo mʼchipululu+ kuti, ‘Musamatsatire malamulo a makolo anu+ kapena kusunga zigamulo zawo kapenanso kudziipitsa ndi mafano awo onyansa.
18 Ndinauza ana awo mʼchipululu+ kuti, ‘Musamatsatire malamulo a makolo anu+ kapena kusunga zigamulo zawo kapenanso kudziipitsa ndi mafano awo onyansa.