-
Ezekieli 20:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma anawo anayamba kundipandukira.+ Sanatsatire malamulo anga ndipo sanasunge komanso kutsatira zigamulo zanga, zimene ngati munthu atazitsatira zingamuthandize kuti akhale ndi moyo. Iwo anadetsa sabata langa. Choncho ine ndinatsimikiza mtima kuti ndiwatsanulire mkwiyo wanga komanso kuwaonetsa ukali wanga wonse mʼchipululu.+
-