-
Ezekieli 20:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana mbali yakumʼmwera ndipo ulankhule zokhudza kumeneko. Ulosere zokhudza nkhalango ya dziko lakumʼmwera.
-