Ezekieli 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uuze dziko la Isiraeli kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ine ndidzakulanga ndipo ndidzasolola lupanga langa mʼchimake+ nʼkupha anthu ako olungama ndiponso anthu ako oipa. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:3 Nsanja ya Olonda,7/1/2007, tsa. 149/15/1988, tsa. 19
3 Uuze dziko la Isiraeli kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ine ndidzakulanga ndipo ndidzasolola lupanga langa mʼchimake+ nʼkupha anthu ako olungama ndiponso anthu ako oipa.