-
Ezekieli 21:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Chifukwa chakuti ndidzapha anthu ako olungama ndi ochimwa, ndidzasolola lupanga langa mʼchimake nʼkupha anthu onse, kuchokera kumʼmwera mpaka kumpoto.
-