Ezekieli 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwe mwana wa munthu, ubuule komanso kunjenjemera. Ubuule pamaso pawo mowawidwa mtima.+