-
Ezekieli 21:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 “Koma iwe mwana wa munthu, jambula msewu umene ukuchokera mʼdzikolo. Pamalo ena msewuwo ugawikane nʼkukhala misewu iwiri. Mfumu ya Babulo imene ikubwera ndi lupanga idzasankha msewu umene ikuyenera kudutsa. Pamphambano pamene misewuyi yagawikana uikepo chikwangwani cholozera* kumene kuli mizindayo.
-