20 Usonyeze kuti msewu umodzi ndi woti mudzadutse lupanga likamadzapita kukawononga mzinda wa Raba+ wa mbadwa za Amoni, ndipo msewu winawo ndi woti lidzadutsemo likamadzapita ku Yuda kukawononga mzinda wa Yerusalemu umene uli ndi mpanda wolimba kwambiri.+