Ezekieli 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa mfumu ya Babulo idzaima pamalo pamene misewu iwiriyo yagawikana kuti iwombeze maula. Mfumuyo idzagwedeza mivi, idzafunsira kwa mafano ake* komanso idzawombeza maula pogwiritsa ntchito chiwindi cha nyama. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:21 Galamukani!,1/2011, tsa. 11 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 19
21 Chifukwa mfumu ya Babulo idzaima pamalo pamene misewu iwiriyo yagawikana kuti iwombeze maula. Mfumuyo idzagwedeza mivi, idzafunsira kwa mafano ake* komanso idzawombeza maula pogwiritsa ntchito chiwindi cha nyama.