Ezekieli 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Bwezerani lupanga mʼchimake. Ndidzakuweruzirani kumalo amene munabadwira,* mʼdziko limene munachokera.
30 Bwezerani lupanga mʼchimake. Ndidzakuweruzirani kumalo amene munabadwira,* mʼdziko limene munachokera.