Ezekieli 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kupereka uthenga wachiweruzo kwa mzinda* umene uli ndi mlandu wa magaziwu+ komanso kuudziwitsa zonyansa zake zonse?+
2 “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kupereka uthenga wachiweruzo kwa mzinda* umene uli ndi mlandu wa magaziwu+ komanso kuudziwitsa zonyansa zake zonse?+