4 magazi amene wakhetsa apangitsa kuti ukhale ndi mlandu+ ndipo mafano ako onyansa apangitsa kuti ukhale wodetsedwa.+ Wafupikitsa masiku a moyo wako ndipo ulangidwa posachedwapa. Nʼchifukwa chake ndachititsa kuti anthu a mitundu ina azikunyoza komanso kuti anthu amʼmayiko onse azikuseka.+