Ezekieli 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mayiko amene uli nawo pafupi ndiponso amene ali kutali ndi iwe adzakuseka,+ iwe amene dzina lako ndi lodetsedwa komanso uli ndi mavuto ambiri.
5 Mayiko amene uli nawo pafupi ndiponso amene ali kutali ndi iwe adzakuseka,+ iwe amene dzina lako ndi lodetsedwa komanso uli ndi mavuto ambiri.