Ezekieli 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Taona! Mtsogoleri aliyense wa Isiraeli pakati pako akugwiritsa ntchito udindo wake kuti akhetse magazi.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:6 Nsanja ya Olonda,8/1/2012, tsa. 27
6 Taona! Mtsogoleri aliyense wa Isiraeli pakati pako akugwiritsa ntchito udindo wake kuti akhetse magazi.+