Ezekieli 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwa iwe muli anthu amene amanyoza bambo awo komanso mayi awo.+ Mlendo amamuchitira zinthu mwachinyengo ndipo amazunza mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.”’”+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:7 Nsanja ya Olonda,8/1/2012, tsa. 27
7 Mwa iwe muli anthu amene amanyoza bambo awo komanso mayi awo.+ Mlendo amamuchitira zinthu mwachinyengo ndipo amazunza mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.”’”+