Ezekieli 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwa iwe muli anthu amiseche amene amafuna kukhetsa magazi.+ Mulinso anthu amene amadya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano mʼmapiri ndipo amachita khalidwe lonyansa pakati panu.+
9 Mwa iwe muli anthu amiseche amene amafuna kukhetsa magazi.+ Mulinso anthu amene amadya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano mʼmapiri ndipo amachita khalidwe lonyansa pakati panu.+