Ezekieli 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi udzapitiriza kukhala wolimba mtima ndipo kodi dzanja lako lidzakhalabe lamphamvu pa tsiku limene ndidzakulange?+ Ine Yehova ndanena ndipo ndidzachitapo kanthu.
14 Kodi udzapitiriza kukhala wolimba mtima ndipo kodi dzanja lako lidzakhalabe lamphamvu pa tsiku limene ndidzakulange?+ Ine Yehova ndanena ndipo ndidzachitapo kanthu.