Ezekieli 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu ako ndidzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndipo ndidzawamwaza mʼmayiko osiyanasiyana.+ Komanso ndidzathetsa khalidwe lako lonyansa.+
15 Anthu ako ndidzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndipo ndidzawamwaza mʼmayiko osiyanasiyana.+ Komanso ndidzathetsa khalidwe lako lonyansa.+