Ezekieli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Iwe mwana wa munthu, kwa ine nyumba ya Isiraeli yakhala ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga zitsulo. Onse ali ngati kopa,* tini, chitsulo ndi mtovu zimene zili mungʼanjo. Iwo akhala ngati zinthu zimene zimatsalira akayenga siliva.+
18 “Iwe mwana wa munthu, kwa ine nyumba ya Isiraeli yakhala ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga zitsulo. Onse ali ngati kopa,* tini, chitsulo ndi mtovu zimene zili mungʼanjo. Iwo akhala ngati zinthu zimene zimatsalira akayenga siliva.+