Ezekieli 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzakusonkhanitsani pamodzi ngati mmene amasonkhanitsira siliva, kopa, chitsulo, mtovu ndi tini mungʼanjo kuti azikolezere moto nʼkuzisungunula. Ndidzachita zimenezi nditakwiya komanso mwaukali ndipo ndidzakukolezerani moto nʼkukusungunulani.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:20 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 20
20 Ndidzakusonkhanitsani pamodzi ngati mmene amasonkhanitsira siliva, kopa, chitsulo, mtovu ndi tini mungʼanjo kuti azikolezere moto nʼkuzisungunula. Ndidzachita zimenezi nditakwiya komanso mwaukali ndipo ndidzakukolezerani moto nʼkukusungunulani.+