Ezekieli 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aneneri ako akukonza chiwembu mʼdzikoli.+ Iwo ali ngati mkango wobangula umene wagwira nyama+ ndipo akupha anthu. Akulanda anthu chuma ndi zinthu zawo zamtengo wapatali. Apangitsa kuti akazi amasiye achuluke mʼdzikolo.
25 Aneneri ako akukonza chiwembu mʼdzikoli.+ Iwo ali ngati mkango wobangula umene wagwira nyama+ ndipo akupha anthu. Akulanda anthu chuma ndi zinthu zawo zamtengo wapatali. Apangitsa kuti akazi amasiye achuluke mʼdzikolo.