Ezekieli 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Akalonga amʼdzikoli ali ngati mimbulu yomwe ikukhadzula nyama. Iwo akukhetsa magazi ndiponso kupha anthu nʼcholinga chopeza phindu mwachinyengo.+
27 Akalonga amʼdzikoli ali ngati mimbulu yomwe ikukhadzula nyama. Iwo akukhetsa magazi ndiponso kupha anthu nʼcholinga chopeza phindu mwachinyengo.+