Ezekieli 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma aneneri amʼdzikomo apaka laimu zochita za akalongawo. Iwo amaona masomphenya onama ndipo amalosera zinthu zabodza.+ Aneneriwo amanena kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,” pamene Yehova sananene chilichonse.
28 Koma aneneri amʼdzikomo apaka laimu zochita za akalongawo. Iwo amaona masomphenya onama ndipo amalosera zinthu zabodza.+ Aneneriwo amanena kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,” pamene Yehova sananene chilichonse.