Ezekieli 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu amʼdzikolo abera anthu mwachinyengo komanso achita zauchifwamba.+ Iwo achitira nkhanza anthu ovutika ndi osauka. Abera mlendo mwachinyengo komanso sanamuchitire zinthu mwachilungamo.’
29 Anthu amʼdzikolo abera anthu mwachinyengo komanso achita zauchifwamba.+ Iwo achitira nkhanza anthu ovutika ndi osauka. Abera mlendo mwachinyengo komanso sanamuchitire zinthu mwachilungamo.’