-
Ezekieli 22:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Choncho ndidzawakhuthulira mkwiyo wanga ndipo ndidzawawononga onse ndi moto wa ukali wanga. Ndidzawalanga mogwirizana ndi zochita zawo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
-