Ezekieli 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akazi amenewa anayamba kuchita uhule mʼdziko la Iguputo.+ Anayamba uhulewu ali atsikana angʼonoangʼono. Kumeneko amuna anafinya mabere awo komanso kusisita pamtima pawo ali anamwali.
3 Akazi amenewa anayamba kuchita uhule mʼdziko la Iguputo.+ Anayamba uhulewu ali atsikana angʼonoangʼono. Kumeneko amuna anafinya mabere awo komanso kusisita pamtima pawo ali anamwali.