Ezekieli 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wamkulu dzina lake anali Ohola,* wamngʼono anali Oholiba.* Akazi amenewa anakhala anga ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi. Ohola akuimira Samariya+ ndipo Oholiba akuimira Yerusalemu. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:4 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 20
4 Wamkulu dzina lake anali Ohola,* wamngʼono anali Oholiba.* Akazi amenewa anakhala anga ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi. Ohola akuimira Samariya+ ndipo Oholiba akuimira Yerusalemu.