Ezekieli 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ohola anayamba kuchita uhule+ ngakhale kuti anali mkazi wanga. Ankalakalaka kugona ndi amuna amene ankamukonda kwambiri+ omwe ndi Asuri amene ankakhala moyandikana naye.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:5 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, ptsa. 20-21
5 Ohola anayamba kuchita uhule+ ngakhale kuti anali mkazi wanga. Ankalakalaka kugona ndi amuna amene ankamukonda kwambiri+ omwe ndi Asuri amene ankakhala moyandikana naye.+