Ezekieli 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mchemwali wake Oholiba ataona zimenezi, chilakolako chake chinafika poipa kwambiri ndipo uhule wake unafika poipa kuposa wa mkulu wake.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:11 Nsanja ya Olonda,4/1/1989, tsa. 30
11 Mchemwali wake Oholiba ataona zimenezi, chilakolako chake chinafika poipa kwambiri ndipo uhule wake unafika poipa kuposa wa mkulu wake.+