-
Ezekieli 23:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma iye anapitiriza kuwonjezera zochita zake zauhule. Iye anaona zithunzi za amuna zogoba pakhoma, zithunzi zogoba za Akasidi zopaka penti yofiira.
-