-
Ezekieli 23:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Anaona zithunzi za amuna atavala malamba mʼchiuno ndipo kumutu kwawo anavala nduwira zazitali zolendewera. Amuna onsewo ankaoneka ngati asilikali komanso ngati amuna a ku Babulo, obadwira mʼdziko la Akasidi.
-