-
Ezekieli 23:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho amuna a ku Babulowo ankabwera pabedi pake nʼkumachita zachikondi ndipo anamuipitsa ndi chiwerewere chawo. Amunawo atamuipitsa, iye anawasiya chifukwa anayamba kunyansidwa nawo.
-