Ezekieli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Oholiba atapitiriza kuchita uhule mopanda manyazi komanso kudzivula,+ ine ndinamusiya chifukwa chonyansidwa naye, ngati mmene ndinasiyira mchemwali wake chifukwa chonyansidwa naye.+
18 Oholiba atapitiriza kuchita uhule mopanda manyazi komanso kudzivula,+ ine ndinamusiya chifukwa chonyansidwa naye, ngati mmene ndinasiyira mchemwali wake chifukwa chonyansidwa naye.+