Ezekieli 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Oholiba anapitiriza kuwonjezera zochita zake zauhule+ mpaka kufika pokumbukira masiku amene anali kamtsikana, pamene ankachita uhule mʼdziko la Iguputo.+
19 Oholiba anapitiriza kuwonjezera zochita zake zauhule+ mpaka kufika pokumbukira masiku amene anali kamtsikana, pamene ankachita uhule mʼdziko la Iguputo.+