-
Ezekieli 23:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Iwo adzabwera kudzakuukira ndipo akamadzabwera, padzamveka phokoso la magaleta ankhondo ndi la mawilo. Adzabwera ndi gulu lalikulu la asilikali, atatenga zishango zazikulu, zishango zazingʼono ndiponso atavala zipewa. Iwo adzakuzungulira ndipo ndidzawapatsa mphamvu zoweruza, moti adzakuweruza mmene akufunira.+
-