Ezekieli 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ine ndidzathetsa khalidwe lako lonyansa ndiponso uhule wako+ umene unauyambira mʼdziko la Iguputo.+ Udzasiya kuyangʼana amuna a ku Iguputo ndipo dziko la Iguputo sudzalikumbukiranso.’
27 Ine ndidzathetsa khalidwe lako lonyansa ndiponso uhule wako+ umene unauyambira mʼdziko la Iguputo.+ Udzasiya kuyangʼana amuna a ku Iguputo ndipo dziko la Iguputo sudzalikumbukiranso.’