Ezekieli 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Adzakuchitira zimenezi chifukwa chakuti unkalakalaka anthu a mitundu ina ngati hule+ komanso chifukwa chakuti unadziipitsa ndi mafano awo onyansa.+
30 Adzakuchitira zimenezi chifukwa chakuti unkalakalaka anthu a mitundu ina ngati hule+ komanso chifukwa chakuti unadziipitsa ndi mafano awo onyansa.+