Ezekieli 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwe udzamwa ndi kugugudiza zamʼkapuyo+ ndipo udzatafuna zidutswa za kapuyoKenako udzakhadzula mabere ako. “Ine ndanena,” akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’
34 Iwe udzamwa ndi kugugudiza zamʼkapuyo+ ndipo udzatafuna zidutswa za kapuyoKenako udzakhadzula mabere ako. “Ine ndanena,” akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’