Ezekieli 23:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti wandiiwala ndipo sukundilabadiranso,*+ udzalangidwa chifukwa cha khalidwe lako lonyansa ndi zochita zako zauhule.’”
35 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti wandiiwala ndipo sukundilabadiranso,*+ udzalangidwa chifukwa cha khalidwe lako lonyansa ndi zochita zako zauhule.’”