Ezekieli 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kupereka uthenga wachiweruzo kwa Ohola ndi Oholiba+ komanso kuwauza zinthu zonyansa zimene achita?
36 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kupereka uthenga wachiweruzo kwa Ohola ndi Oholiba+ komanso kuwauza zinthu zonyansa zimene achita?