Ezekieli 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atapha ana awo aamuna nʼkuwapereka nsembe kwa mafano onyansa,+ tsiku lomwelo anabwera kumalo anga opatulika kudzawadetsa.+ Izi ndi zimene anachita mʼnyumba yanga.
39 Atapha ana awo aamuna nʼkuwapereka nsembe kwa mafano onyansa,+ tsiku lomwelo anabwera kumalo anga opatulika kudzawadetsa.+ Izi ndi zimene anachita mʼnyumba yanga.