Ezekieli 23:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kuwonjezera apo, akaziwo anatumiza uthenga kwa amuna ochokera kutali kuti abwere.+ Amunawo akubwera, iwe unasamba nʼkupaka zodzikongoletsera mʼmaso mwako ndipo unavala zodzikongoletsera.+
40 Kuwonjezera apo, akaziwo anatumiza uthenga kwa amuna ochokera kutali kuti abwere.+ Amunawo akubwera, iwe unasamba nʼkupaka zodzikongoletsera mʼmaso mwako ndipo unavala zodzikongoletsera.+