Ezekieli 23:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Kenako unakhala pampando wabwino kwambiri+ ndipo patsogolo pake panali tebulo loyalidwa bwino.+ Patebulopo unaikapo zofukiza zanga zonunkhira+ komanso mafuta anga.+
41 Kenako unakhala pampando wabwino kwambiri+ ndipo patsogolo pake panali tebulo loyalidwa bwino.+ Patebulopo unaikapo zofukiza zanga zonunkhira+ komanso mafuta anga.+